2 Mbiri 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anamanganso mzinda wa Beti-horoni+ Wakumtunda ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, mageti ndi mipiringidzo.
5 Anamanganso mzinda wa Beti-horoni+ Wakumtunda ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, mageti ndi mipiringidzo.