6 Anamanganso Baalati+ ndi mizinda yonse yosungirako zinthu ya Solomo, mizinda yonse yosungirako magaleta,+ mizinda ya amuna okwera pamahatchi ndiponso zilizonse zimene iye anafuna kumanga ku Yerusalemu, ku Lebanoni ndi mʼmadera onse amene ankalamulira.