2 Mbiri 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 komanso mbadwa zawo zimene zinatsala mʼdzikomo, zomwe Aisiraeli analephera kuzipha.+ Anthu onsewa Solomo ankawagwiritsa ntchito yaukapolo ndipo akugwirabe ntchitoyi mpaka lero.+
8 komanso mbadwa zawo zimene zinatsala mʼdzikomo, zomwe Aisiraeli analephera kuzipha.+ Anthu onsewa Solomo ankawagwiritsa ntchito yaukapolo ndipo akugwirabe ntchitoyi mpaka lero.+