2 Mbiri 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma palibe Aisiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo ogwira ntchito yake,+ chifukwa iwo anali asilikali ake, atsogoleri a asilikali ake othandiza pamagaleta ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta ndi amuna okwera pamahatchi.+
9 Koma palibe Aisiraeli amene Solomo anawasandutsa akapolo ogwira ntchito yake,+ chifukwa iwo anali asilikali ake, atsogoleri a asilikali ake othandiza pamagaleta ndiponso atsogoleri a asilikali ake oyendetsa magaleta ndi amuna okwera pamahatchi.+