2 Mbiri 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma sindinakhulupirire zimene ndinauzidwa mpaka pamene ndabwera nʼkuona ndi maso anga.+ Panopa ndaona kuti zimene ndinauzidwa zinali hafu chabe ya nzeru zanu zambiri.+ Mwaposa kwambiri zimene ndinamva.+
6 Koma sindinakhulupirire zimene ndinauzidwa mpaka pamene ndabwera nʼkuona ndi maso anga.+ Panopa ndaona kuti zimene ndinauzidwa zinali hafu chabe ya nzeru zanu zambiri.+ Mwaposa kwambiri zimene ndinamva.+