9 Kenako mfumukaziyo inapatsa mfumuyo golide wokwana matalente 120,+ mafuta a basamu ochuluka kwambiri ndiponso miyala yamtengo wapatali. Mafuta a basamu amene mfumukazi ya ku Sheba inapatsa Mfumu Solomo, anali ambiri moti sipanakhalenso mafuta ochuluka choncho.+