2 Mbiri 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kuwonjezera pamenepo, atumiki a Hiramu ndi atumiki a Solomo amene anabwera ndi golide kuchokera ku Ofiri,+ anabweretsanso matabwa a mtengo wa mʼbawa ndi miyala yamtengo wapatali.+
10 Kuwonjezera pamenepo, atumiki a Hiramu ndi atumiki a Solomo amene anabwera ndi golide kuchokera ku Ofiri,+ anabweretsanso matabwa a mtengo wa mʼbawa ndi miyala yamtengo wapatali.+