2 Mbiri 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 osawerengera golide wochokera kwa amalonda oyendayenda ndi amalonda ena, komanso wochokera kwa mafumu onse a Aluya ndi kwa abwanamkubwa amʼdzikolo, amene ankabweretsa golide ndi siliva kwa Solomo.+
14 osawerengera golide wochokera kwa amalonda oyendayenda ndi amalonda ena, komanso wochokera kwa mafumu onse a Aluya ndi kwa abwanamkubwa amʼdzikolo, amene ankabweretsa golide ndi siliva kwa Solomo.+