2 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mfumuyo inapanganso mpando wachifumu waukulu waminyanga ya njovu nʼkuukuta ndi golide woyenga bwino.+
17 Mfumuyo inapanganso mpando wachifumu waukulu waminyanga ya njovu nʼkuukuta ndi golide woyenga bwino.+