2 Mbiri 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Panali masitepe 6 okafika kumpando wachifumuwo. Mpando wachifumuwo unali ndi chopondapo mapazi chagolide cholumikiza kumpandowo. Mpandowo unali ndi moika manja mbali zonse ziwiri. Mʼmbali mwake munali zifaniziro ziwiri za mikango+ itaimirira.
18 Panali masitepe 6 okafika kumpando wachifumuwo. Mpando wachifumuwo unali ndi chopondapo mapazi chagolide cholumikiza kumpandowo. Mpandowo unali ndi moika manja mbali zonse ziwiri. Mʼmbali mwake munali zifaniziro ziwiri za mikango+ itaimirira.