2 Mbiri 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamasitepe 6 aja, panali zifaniziro 12 za mikango+ itaimirira. Kumapeto kwa sitepe iliyonse kunali mkango umodzi. Panalibenso ufumu womwe unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.
19 Pamasitepe 6 aja, panali zifaniziro 12 za mikango+ itaimirira. Kumapeto kwa sitepe iliyonse kunali mkango umodzi. Panalibenso ufumu womwe unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.