2 Mbiri 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mafumu onse apadziko lapansi ankafuna kuonana ndi Solomo kuti amve nzeru zake zimene Mulungu woona anaika mumtima mwake.+
23 Mafumu onse apadziko lapansi ankafuna kuonana ndi Solomo kuti amve nzeru zake zimene Mulungu woona anaika mumtima mwake.+