2 Mbiri 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthuwo ankabweretsa mphatso monga zinthu zasiliva, zinthu zagolide, zovala,+ zida zankhondo, mafuta a basamu, mahatchi komanso nyulu* ndipo zimenezi zinkachitika chaka chilichonse.
24 Anthuwo ankabweretsa mphatso monga zinthu zasiliva, zinthu zagolide, zovala,+ zida zankhondo, mafuta a basamu, mahatchi komanso nyulu* ndipo zimenezi zinkachitika chaka chilichonse.