2 Mbiri 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Solomo,+ kuyambira zoyamba mpaka zomaliza, zikupezeka mʼzinthu zimene mneneri Natani+ analemba, mu ulosi wa Ahiya+ wa ku Silo ndiponso mʼbuku la masomphenya a mneneri* Ido,+ lonena za Yerobowamu+ mwana wa Nebati. 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:29 Nsanja ya Olonda,2/15/2012, tsa. 25
29 Nkhani zina zokhudza Solomo,+ kuyambira zoyamba mpaka zomaliza, zikupezeka mʼzinthu zimene mneneri Natani+ analemba, mu ulosi wa Ahiya+ wa ku Silo ndiponso mʼbuku la masomphenya a mneneri* Ido,+ lonena za Yerobowamu+ mwana wa Nebati.