2 Mbiri 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Solomo, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide bambo ake.+ Ndiyeno mwana wake Rehobowamu, anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
31 Kenako Solomo, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide bambo ake.+ Ndiyeno mwana wake Rehobowamu, anakhala mfumu mʼmalo mwake.+