2 Mbiri 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Bambo anu anachititsa kuti goli lathu likhale lowawa.+ Koma inuyo mukatifewetsera ntchito yowawa ya bambo anu komanso goli lolemera limene ankatisenzetsa, tizikutumikirani.” 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2018, tsa. 13
4 “Bambo anu anachititsa kuti goli lathu likhale lowawa.+ Koma inuyo mukatifewetsera ntchito yowawa ya bambo anu komanso goli lolemera limene ankatisenzetsa, tizikutumikirani.”