2 Mbiri 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iye sanamvere malangizo amene anthu achikulirewo* anamupatsa, ndipo anapita kukafunsira malangizo kwa achinyamata amene anakulira naye limodzi, omwe ankamutumikira.+
8 Koma iye sanamvere malangizo amene anthu achikulirewo* anamupatsa, ndipo anapita kukafunsira malangizo kwa achinyamata amene anakulira naye limodzi, omwe ankamutumikira.+