-
2 Mbiri 10:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Achinyamata amene anakulira naye limodziwo anamuuza kuti: “Anthu amene akuuzani kuti, ‘Bambo anu anatisenzetsa goli lolemera, koma inuyo mutipeputsirekoʼ mukawauze kuti, ‘Chala changa chachingʼono chidzakhala chachikulu kuposa chiuno cha bambo anga.
-