2 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mfumuyo inawayankha mwaukali. Ndipo Mfumu Rehobowamu sanamvere malangizo a anthu achikulire* aja.
13 Koma mfumuyo inawayankha mwaukali. Ndipo Mfumu Rehobowamu sanamvere malangizo a anthu achikulire* aja.