-
2 Mbiri 10:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Inayankha anthuwo motsatira malangizo a achinyamata aja. Inati: “Ine ndidzachititsa kuti goli lanu likhale lolemera kwambiri, ndipo ndidzaliwonjezera. Bambo anga ankakukwapulani ndi zikwapu koma ineyo ndizikukwapulani ndi zikoti zaminga.”
-