2 Mbiri 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho mfumu sinamvere anthuwo. Mulungu woona+ ndi amene anachititsa kuti zinthu zikhale chonchi, kuti akwaniritse mawu amene Yehova analankhula kwa Yerobowamu mwana wa Nebati kudzera mwa Ahiya+ wa ku Silo.
15 Choncho mfumu sinamvere anthuwo. Mulungu woona+ ndi amene anachititsa kuti zinthu zikhale chonchi, kuti akwaniritse mawu amene Yehova analankhula kwa Yerobowamu mwana wa Nebati kudzera mwa Ahiya+ wa ku Silo.