-
2 Mbiri 10:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Aisiraeli onse ataona kuti mfumuyo yakana kuwamvera, anayankha kuti: “Ife Davide tilibe naye ntchito ndipo sitingapatsidwe cholowa kuchokera kwa mwana wa Jese. Aisiraeli inu, aliyense apite kwa milungu yake! Tsopano iwe Davide,+ uziyangʼanira nyumba yako yokha.” Zitatero, Aisiraeli onsewo anabwerera kunyumba* kwawo.+
-