2 Mbiri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma Aisiraeli anamugenda ndi miyala nʼkumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta lake nʼkuthawira ku Yerusalemu.+
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Hadoramu+ amene ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma Aisiraeli anamugenda ndi miyala nʼkumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta lake nʼkuthawira ku Yerusalemu.+