2 Mbiri 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Rehobowamu atangofika ku Yerusalemu, anasonkhanitsa asilikali ophunzitsidwa bwino* okwana 180,000 a nyumba yonse ya Yuda ndi fuko la Benjamini.+ Anawasonkhanitsa kuti akamenyane ndi Aisiraeli kuti ufumu ubwerere kwa Rehobowamu.+
11 Rehobowamu atangofika ku Yerusalemu, anasonkhanitsa asilikali ophunzitsidwa bwino* okwana 180,000 a nyumba yonse ya Yuda ndi fuko la Benjamini.+ Anawasonkhanitsa kuti akamenyane ndi Aisiraeli kuti ufumu ubwerere kwa Rehobowamu.+