2 Mbiri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Yehova wanena kuti: “Musapite kukamenyana ndi abale anu. Aliyense abwerere kunyumba kwawo chifukwa ine ndi amene ndachititsa zimenezi.”’”+ Choncho anthuwo anamvera mawu a Yehova nʼkubwerera kwawo ndipo sanapite kukamenyana ndi Yerobowamu.
4 ‘Yehova wanena kuti: “Musapite kukamenyana ndi abale anu. Aliyense abwerere kunyumba kwawo chifukwa ine ndi amene ndachititsa zimenezi.”’”+ Choncho anthuwo anamvera mawu a Yehova nʼkubwerera kwawo ndipo sanapite kukamenyana ndi Yerobowamu.