-
2 Mbiri 11:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kuwonjezera pamenepo, analimbitsanso malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri nʼkuikamo atsogoleri. Atatero mʼmizindamo anaikamo chakudya, mafuta ndi vinyo.
-