2 Mbiri 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto ndi madera awo+ nʼkupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu, chifukwa Yerobowamu ndi ana ake anachotsa Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.+
14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto ndi madera awo+ nʼkupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu, chifukwa Yerobowamu ndi ana ake anachotsa Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.+