2 Mbiri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yerobowamu anaika ansembe ake mʼmalo okwezeka+ kuti azitumikira ziwanda+ zooneka ngati mbuzi* ndi mafano a ana a ngʼombe amene iye anapanga.+
15 Kenako Yerobowamu anaika ansembe ake mʼmalo okwezeka+ kuti azitumikira ziwanda+ zooneka ngati mbuzi* ndi mafano a ana a ngʼombe amene iye anapanga.+