2 Mbiri 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma anthu a mʼmafuko onse a Isiraeli amene anali ndi mtima wofunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli, anatsatira ansembe ku Yerusalemu kukapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+
16 Koma anthu a mʼmafuko onse a Isiraeli amene anali ndi mtima wofunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli, anatsatira ansembe ku Yerusalemu kukapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+