2 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼchaka cha 5 cha Mfumu Rehobowamu, Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu, chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova.
2 Mʼchaka cha 5 cha Mfumu Rehobowamu, Sisaki+ mfumu ya Iguputo anabwera kudzaukira Yerusalemu, chifukwa iwo anachita zosakhulupirika kwa Yehova.