2 Mbiri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anabwera kuchokera ku Iguputo ndi magaleta 1,200, amuna okwera pamahatchi 60,000 komanso anthu osawerengeka. Anthuwo anali Alibiya, Asuki ndi Aitiyopiya.+
3 Anabwera kuchokera ku Iguputo ndi magaleta 1,200, amuna okwera pamahatchi 60,000 komanso anthu osawerengeka. Anthuwo anali Alibiya, Asuki ndi Aitiyopiya.+