2 Mbiri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mneneri Semaya+ anapita kwa Rehobowamu ndi kwa akalonga a Yuda amene anasonkhana ku Yerusalemu chifukwa cha Sisaki nʼkuwauza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Inuyo mwandisiya, choncho inenso ndakusiyani+ ndipo ndakuperekani mʼmanja mwa Sisaki.’”
5 Mneneri Semaya+ anapita kwa Rehobowamu ndi kwa akalonga a Yuda amene anasonkhana ku Yerusalemu chifukwa cha Sisaki nʼkuwauza kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Inuyo mwandisiya, choncho inenso ndakusiyani+ ndipo ndakuperekani mʼmanja mwa Sisaki.’”