2 Mbiri 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Sisaki mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu. Iye anatenga chuma chamʼnyumba ya Yehova+ ndi chuma chamʼnyumba ya mfumu. Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:9 Nsanja ya Olonda,2/1/1988, tsa. 26
9 Choncho Sisaki mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu. Iye anatenga chuma chamʼnyumba ya Yehova+ ndi chuma chamʼnyumba ya mfumu. Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+