2 Mbiri 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa chakuti mfumu inadzichepetsa, Yehova anabweza mkwiyo wake+ ndipo sanawononge anthu onsewo.+ Komanso anapeza kuti panali zinthu zina zabwino zomwe anthu a ku Yuda ankachita.+
12 Chifukwa chakuti mfumu inadzichepetsa, Yehova anabweza mkwiyo wake+ ndipo sanawononge anthu onsewo.+ Komanso anapeza kuti panali zinthu zina zabwino zomwe anthu a ku Yuda ankachita.+