-
2 Mbiri 12:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mfumu Rehobowamu inalimbitsa ufumu wake ku Yerusalemu ndipo inapitiriza kulamulira. Rehobowamu anali ndi zaka 41 pamene ankayamba kulamulira, ndipo analamulira kwa zaka 17 ku Yerusalemu, mzinda umene Yehova anasankha pa mafuko onse a Isiraeli kuti kukhale dzina lake. Mayi ake anali Naama, mbadwa ya Amoni.+
-