15 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu, kuyambira zoyamba mpaka zomaliza, zikupezeka mʼzimene analemba mneneri Semaya+ ndiponso Ido+ wamasomphenya, motsatira mndandanda wa mayina a makolo. Pakati pa Rehobowamu ndi Yerobowamu pankachitika nkhondo nthawi zonse.+