3 Choncho Abiya anapita kunkhondoko ndi gulu la asilikali amphamvu komanso ophunzitsidwa bwino okwana 400,000.+ Nayenso Yerobowamu anapita kukamenyana ndi Abiya ndipo anapita ndi asilikali 800,000 amphamvu komanso ophunzitsidwa bwino, ndipo anali okonzeka kumenya nkhondo.