2 Mbiri 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi simukudziwa kuti Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka ufumu kwa Davide kuti azilamulira Isiraeli mpaka kalekale?+ Simukudziwa kodi kuti anaupereka kwa iye ndi ana ake+ pochita naye pangano la mchere?*+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:5 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, tsa. 20
5 Kodi simukudziwa kuti Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka ufumu kwa Davide kuti azilamulira Isiraeli mpaka kalekale?+ Simukudziwa kodi kuti anaupereka kwa iye ndi ana ake+ pochita naye pangano la mchere?*+