2 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mukuganiza zolimbana ndi ufumu wa Yehova umene uli mʼmanja mwa ana a Davide, chifukwa chakuti mulipo ambiri komanso muli ndi ana a ngʼombe agolide amene Yerobowamu anakupangirani kuti akhale milungu yanu.+
8 Tsopano mukuganiza zolimbana ndi ufumu wa Yehova umene uli mʼmanja mwa ana a Davide, chifukwa chakuti mulipo ambiri komanso muli ndi ana a ngʼombe agolide amene Yerobowamu anakupangirani kuti akhale milungu yanu.+