2 Mbiri 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ife, Mulungu wathu ndi Yehova+ ndipo sitinamusiye. Ansembe athu, omwe ndi mbadwa za Aroni, akutumikira Yehova, ndipo Alevi akuthandiza pa ntchitoyi.
10 Koma ife, Mulungu wathu ndi Yehova+ ndipo sitinamusiye. Ansembe athu, omwe ndi mbadwa za Aroni, akutumikira Yehova, ndipo Alevi akuthandiza pa ntchitoyi.