2 Mbiri 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Abiya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide.+ Ndiyeno mwana wake Asa anakhala mfumu mʼmalo mwake. Mʼmasiku ake, mʼdzikomo munali mtendere kwa zaka 10.
14 Kenako Abiya, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide.+ Ndiyeno mwana wake Asa anakhala mfumu mʼmalo mwake. Mʼmasiku ake, mʼdzikomo munali mtendere kwa zaka 10.