2 Mbiri 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anachotsa maguwa ansembe achilendo,+ anagwetsa malo okwezeka, anaphwanya zipilala zopatulika+ komanso anagwetsa mizati yopatulika.*+ 2 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:3 Nsanja ya Olonda,6/15/2009, tsa. 12
3 Iye anachotsa maguwa ansembe achilendo,+ anagwetsa malo okwezeka, anaphwanya zipilala zopatulika+ komanso anagwetsa mizati yopatulika.*+