2 Mbiri 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anachotsa malo okwezeka ndi maguwa operekera nsembe zonunkhira+ mʼmizinda yonse ya Yuda, ndipo ufumu wake unapitiriza kukhala wopanda chosokoneza chilichonse.
5 Iye anachotsa malo okwezeka ndi maguwa operekera nsembe zonunkhira+ mʼmizinda yonse ya Yuda, ndipo ufumu wake unapitiriza kukhala wopanda chosokoneza chilichonse.