2 Mbiri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko la Yuda,+ chifukwa mʼdzikolo munalibe chosokoneza chilichonse komanso munalibe nkhondo pa zaka zimenezi, chifukwa Yehova anamʼpatsa mpumulo.+
6 Anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko la Yuda,+ chifukwa mʼdzikolo munalibe chosokoneza chilichonse komanso munalibe nkhondo pa zaka zimenezi, chifukwa Yehova anamʼpatsa mpumulo.+