2 Mbiri 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asa anali ndi asilikali 300,000 a fuko la Yuda onyamula zishango zazikulu ndi mikondo ingʼonoingʼono. Analinso ndi asilikali amphamvu okwana 280,000 a fuko la Benjamini onyamula mauta* ndi zishango zazingʼono.*+
8 Asa anali ndi asilikali 300,000 a fuko la Yuda onyamula zishango zazikulu ndi mikondo ingʼonoingʼono. Analinso ndi asilikali amphamvu okwana 280,000 a fuko la Benjamini onyamula mauta* ndi zishango zazingʼono.*+