-
2 Mbiri 14:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iwo anawononganso mizinda yonse yozungulira Gerari chifukwa Yehova anachititsa kuti anthu amʼmizindayo akhale ndi mantha. Anatenga katundu wamʼmizinda yonseyo, chifukwa munali zinthu zambiri zoti angatenge.
-