2 Mbiri 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ali pa mavutowo, anabwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli nʼkumufunafuna, ndipo iye analola kuti amupeze.+
4 Koma ali pa mavutowo, anabwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli nʼkumufunafuna, ndipo iye analola kuti amupeze.+