2 Mbiri 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mtundu unkamenyana ndi mtundu wina ndiponso mzinda ndi mzinda wina, chifukwa Mulungu anawasiya kuti asokonezeke ndi mavuto osiyanasiyana.+
6 Mtundu unkamenyana ndi mtundu wina ndiponso mzinda ndi mzinda wina, chifukwa Mulungu anawasiya kuti asokonezeke ndi mavuto osiyanasiyana.+