-
2 Mbiri 15:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Asa atangomva mawu amenewa komanso ulosi wa mneneri Odedi, analimba mtima nʼkuyamba kuchotsa mafano onyansa mʼdziko lonse la Yuda+ ndi la Benjamini ndiponso mʼmizinda imene analanda mʼdera lamapiri la Efuraimu. Anabwezeretsanso guwa lansembe la Yehova limene linali patsogolo pa khonde la nyumba ya Yehova.+
-