2 Mbiri 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero anasonkhanitsa anthu onse a fuko la Yuda ndi la Benjamini ndiponso alendo ambirimbiri ochokera ku fuko la Efuraimu, la Manase ndi la Simiyoni.+ Alendowa anachoka ku Isiraeli nʼkubwera kwa iye ataona kuti Yehova Mulungu wake ali naye.
9 Atatero anasonkhanitsa anthu onse a fuko la Yuda ndi la Benjamini ndiponso alendo ambirimbiri ochokera ku fuko la Efuraimu, la Manase ndi la Simiyoni.+ Alendowa anachoka ku Isiraeli nʼkubwera kwa iye ataona kuti Yehova Mulungu wake ali naye.